Radio Maria Malawi - FM 99.2 - Blantyre

Save this radio to your Streema Favorites

Ads by Google AdSense

Radio Maria Malawi Info

Play

Get the live Radio Widget

1.5/5 based on 2 reviews. Rate this station

492 Tune Ins

Listen to Ause ndi Mtendere, Mauthenga Ochokera, or shows including Ulimi wa Phindu, in addition to others.

Visit the Radio's website

Religious FM 99.2 32Kbps Italian

Wall

Guest

Guest

kumverA RADIO MARIA MU OFC ON LINE SO NICE

April 11, 2014, 11:39 a.m. GMT

Guest

Guest

kunvera Radio kuno ku South Sudan, ambuye ndi wabwino nthawi zonse. Evaristo Dira wa ku Mozambique.

March 30, 2014, 5:04 a.m. GMT

Guest

Guest

Ndikumvera radio Maria Malawi kudzera pa internet kuno ku Maputo-Mozambique, kundikumbutsa ku Mudzi kwathu ku Mulanje... Mulungu akudalitseni abale nonse ku Malawi

March 7, 2014, 8:25 a.m. GMT

Guest

Guest

Looking 4 my relatives.My father was born in 1937 in Rumphi,Chief Mtwalo's area.We lastly contacted w our relatives in 1984 e address was Chinombo Estate 187Rumphi,Malawi .addressed to kambanizithe chinombo n Peter nkonjera

Feb. 10, 2014, 5:27 p.m. GMT

Guest

Guest

ndikumvera radio malawi ndiri kutali zosangalasa zedi kuno ku kenya

Jan. 22, 2014, 5:56 p.m. GMT

zibach

zibach

Listening to Radio Maria Malawi in Australia.Ambuye ndi wabwino tanwizonse

Nov. 24, 2013, 3:07 a.m. GMT

Guest

Guest

radio Maria phamba wauzimu owona oleka kukonda kugwilitsa tchoto radio yi aganize mofatsa pitilizani kutumikila mlungu Radio maria pemphero {ambuye yesu sithani mintima yawanthu okana kulondola inu osazindikila mphamvu yanu adziwitseni ndithu mulungu wa anthu onse tivekeni kolona wachipulumutso see more... chosatha pakutilalikila ndikutiuza kudzela pa radio yi amen} INE STRANGER CHAZEMBA KU ST MONTFRONT KALIYATI THAMBI YA KADIKILA PARISH KU CHILEKA

Oct. 30, 2013, 6:41 a.m. GMT

Guest

Guest

Ndimasangalala kwambiri ndikamvera Radio Malia Malawi chifukwa yandithandiza pa moyo wanga wauzimu ndipo yazamitsa chikhirisitu changa makamaka nthawi ya ulaliki,Ndine Steven Chinsendenji st vincent de paul parish Blantyre.

Sept. 27, 2013, 10:03 a.m. GMT

Guest

Guest

ndine osangalala pakuti ndili odalitsika pakuvela radio maria malawi Ndikudalitsika m'muzimu m'moona ndithu ndipo m'tima wanga osangalala povera nyimbo za makwaya ndi mapemphero a korona. INE STRANGER CHAZEMBA KU ST MONTFONT KALIYATI NTHAMBI YA KADIKILA PALISH KU CHILEKA

Sept. 22, 2013, 1:39 p.m. GMT

Guest

Guest

musadzaleke radio maria malawi kutumikila mlungu chifukwa ife tikutsitsimuka nanu Stranger chazemba kwa kadikila palish

Sept. 22, 2013, 10:26 a.m. GMT

Reviews - Rate this station:

Guest

ALLAN ZAKEYU MSOSA ine wapampando wa kuno ku RSA Cape town st anthoney mpakati tikukufunilani zabwino zonse pomatipasila maprgm othandiza kukweza/komanso kusinthika kwa moyo wathu wachikhrist.timakunyadilani nthawi zomse

Guest

LINOH KUNO KU RSA AMZANGA ONSE AMENE MULUNGU ANAKUPASANI LUSO LOYIMBA KWEZANI UFUMU WAMULUNGU,MAKAMAKA MAKWAYA.MONI KWA AKHRISTU ONSE KWAMPUNGA LIMBE PARISH,OSAIWALA MAIN CHOIR.

Sign Up for Streema

If you want to save the Radio Maria Malawi live stream, start sharing stations with friends, or engage in a deeper Streema experience, please sign up below.

By clicking Sign up, you are indicating that you have read and agree to the Terms of Service and Privacy Policy.

Streema Mobile

We've developed a mobile website for iOS (iPhone, iPad, iPod) and Android devices. Native apps coming soon!

You can check it out by visiting our mobile radio site from your phone or tablet's mobile browser - it's free, no download required.

For more information go to our Mobile Support .

In other languages

See this page in French: Ecouter Radio Maria Malawi en ligne

Playlist, tracklist, top songs played coming soon...

PC requires Windows Media Player - Mac additionally requires Real Player - See FAQs for more info on how to listen to live streaming radio.